×

M’nyumba zimene Mulungu adalamula kuti zimangidwe ndipo m’menemo dzina lake limakumbukirika, Mulungu 24:36 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah An-Nur ⮕ (24:36) ayat 36 in Chichewa

24:36 Surah An-Nur ayat 36 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah An-Nur ayat 36 - النور - Page - Juz 18

﴿فِي بُيُوتٍ أَذِنَ ٱللَّهُ أَن تُرۡفَعَ وَيُذۡكَرَ فِيهَا ٱسۡمُهُۥ يُسَبِّحُ لَهُۥ فِيهَا بِٱلۡغُدُوِّ وَٱلۡأٓصَالِ ﴾
[النور: 36]

M’nyumba zimene Mulungu adalamula kuti zimangidwe ndipo m’menemo dzina lake limakumbukirika, Mulungu amalemekezeka m’menemo m’mawa ndi madzulo

❮ Previous Next ❯

ترجمة: في بيوت أذن الله أن ترفع ويذكر فيها اسمه يسبح له فيها, باللغة نيانجا

﴿في بيوت أذن الله أن ترفع ويذكر فيها اسمه يسبح له فيها﴾ [النور: 36]

Khaled Ibrahim Betala
“(Apezeke akupemphera kasanu) m’nyumba zomwe Allah walamula kuti zilemekezedwe; ndipo m’menemo dzina Lake litchulidwe; azimulemekeza m’menemo (m’misikiti) kum’mawa ndi kumadzulo
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek