×

Pali anthu amene malonda kapena zogulitsa sizingathe kuwaiwalitsa kukumbukira Mulungu kapena kupemphera 24:37 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah An-Nur ⮕ (24:37) ayat 37 in Chichewa

24:37 Surah An-Nur ayat 37 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah An-Nur ayat 37 - النور - Page - Juz 18

﴿رِجَالٞ لَّا تُلۡهِيهِمۡ تِجَٰرَةٞ وَلَا بَيۡعٌ عَن ذِكۡرِ ٱللَّهِ وَإِقَامِ ٱلصَّلَوٰةِ وَإِيتَآءِ ٱلزَّكَوٰةِ يَخَافُونَ يَوۡمٗا تَتَقَلَّبُ فِيهِ ٱلۡقُلُوبُ وَٱلۡأَبۡصَٰرُ ﴾
[النور: 37]

Pali anthu amene malonda kapena zogulitsa sizingathe kuwaiwalitsa kukumbukira Mulungu kapena kupemphera kapena kupereka msonkho wothandiza anthu osauka. Iwo amene amaopa tsiku limene mitima ndi maso adzatembenuka

❮ Previous Next ❯

ترجمة: رجال لا تلهيهم تجارة ولا بيع عن ذكر الله وإقام الصلاة وإيتاء, باللغة نيانجا

﴿رجال لا تلهيهم تجارة ولا بيع عن ذكر الله وإقام الصلاة وإيتاء﴾ [النور: 37]

Khaled Ibrahim Betala
“Anthu omwe malonda ogulitsa ndi kugula sawatangwanitsa posiya kukumbukira Allah ndi kupemphera (Swala) ndi kupereka chopereka (Zakaat) naopa tsiku lomwe mitima ndi maso zidzatembenukatembenuka
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek