Quran with Chichewa translation - Surah Al-Furqan ayat 33 - الفُرقَان - Page - Juz 19
﴿وَلَا يَأۡتُونَكَ بِمَثَلٍ إِلَّا جِئۡنَٰكَ بِٱلۡحَقِّ وَأَحۡسَنَ تَفۡسِيرًا ﴾
[الفُرقَان: 33]
﴿ولا يأتونك بمثل إلا جئناك بالحق وأحسن تفسيرا﴾ [الفُرقَان: 33]
Khaled Ibrahim Betala “Ndipo sangakubweretsere fanizo lililonse koma tikubweretsera choonadi (choyankha fanizolo ndi kukudziwitsa) ndi kumasulira kwabwino |