Quran with Chichewa translation - Surah Al-Furqan ayat 32 - الفُرقَان - Page - Juz 19
﴿وَقَالَ ٱلَّذِينَ كَفَرُواْ لَوۡلَا نُزِّلَ عَلَيۡهِ ٱلۡقُرۡءَانُ جُمۡلَةٗ وَٰحِدَةٗۚ كَذَٰلِكَ لِنُثَبِّتَ بِهِۦ فُؤَادَكَۖ وَرَتَّلۡنَٰهُ تَرۡتِيلٗا ﴾
[الفُرقَان: 32]
﴿وقال الذين كفروا لولا نـزل عليه القرآن جملة واحدة كذلك لنثبت به﴾ [الفُرقَان: 32]
Khaled Ibrahim Betala “Ndipo amene sadakhulupirire akunena: “Bwanji Qur’an yonse siidavumbulutsidwe nthawi imodzi kwa iye? Momwemo (ukuoneramo, tikuitumiza pang’onopang’ono) kuti tiulimbikitse mtima wako ndi iyo, ndipo taiyala, mkayalidwe kabwino |