×

“Nanga ndi chifukwa chiyani sadapatsidwe chuma ndipo alibe munda woti azipezako chakudya?” 25:8 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Al-Furqan ⮕ (25:8) ayat 8 in Chichewa

25:8 Surah Al-Furqan ayat 8 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Al-Furqan ayat 8 - الفُرقَان - Page - Juz 18

﴿أَوۡ يُلۡقَىٰٓ إِلَيۡهِ كَنزٌ أَوۡ تَكُونُ لَهُۥ جَنَّةٞ يَأۡكُلُ مِنۡهَاۚ وَقَالَ ٱلظَّٰلِمُونَ إِن تَتَّبِعُونَ إِلَّا رَجُلٗا مَّسۡحُورًا ﴾
[الفُرقَان: 8]

“Nanga ndi chifukwa chiyani sadapatsidwe chuma ndipo alibe munda woti azipezako chakudya?” Ndipo anthu ochita zoipa amati, “Ndithudi munthu amene muli kumutsatira ndi wolodzedwa.”

❮ Previous Next ❯

ترجمة: أو يلقى إليه كنـز أو تكون له جنة يأكل منها وقال الظالمون, باللغة نيانجا

﴿أو يلقى إليه كنـز أو تكون له جنة يأكل منها وقال الظالمون﴾ [الفُرقَان: 8]

Khaled Ibrahim Betala
““Kapena kuponyeredwa nkhokwe (za chuma), kapena kukhala ndi munda ndikumadya m’menemo?” Ndipo osalungama akuti: “Ndithudi, mukutsatira munthu wolodzedwa.”
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek