Quran with Chichewa translation - Surah Ash-Shu‘ara’ ayat 42 - الشعراء - Page - Juz 19
﴿قَالَ نَعَمۡ وَإِنَّكُمۡ إِذٗا لَّمِنَ ٱلۡمُقَرَّبِينَ ﴾ 
[الشعراء: 42]
﴿قال نعم وإنكم إذا لمن المقربين﴾ [الشعراء: 42]
| Khaled Ibrahim Betala “(Farawo) adati: “Inde, (ndipo kuonjezera apo) ndithu inu mudzakhala mwa amene amakhala pafupi (ndi ine, monga nduna zanga).” |