Quran with Chichewa translation - Surah An-Naml ayat 11 - النَّمل - Page - Juz 19
﴿إِلَّا مَن ظَلَمَ ثُمَّ بَدَّلَ حُسۡنَۢا بَعۡدَ سُوٓءٖ فَإِنِّي غَفُورٞ رَّحِيمٞ ﴾
[النَّمل: 11]
﴿إلا من ظلم ثم بدل حسنا بعد سوء فإني غفور رحيم﴾ [النَّمل: 11]
Khaled Ibrahim Betala ““Koma amene wadzichitira yekha zoipa, kenako nkusintha (pochita) zabwino pambuyo pa zoipa, (ndimkhululukira) pakuti Ine ndine Wokhululuka kwabasi, Wachifundo chambiri.” |