Quran with Chichewa translation - Surah An-Naml ayat 17 - النَّمل - Page - Juz 19
﴿وَحُشِرَ لِسُلَيۡمَٰنَ جُنُودُهُۥ مِنَ ٱلۡجِنِّ وَٱلۡإِنسِ وَٱلطَّيۡرِ فَهُمۡ يُوزَعُونَ ﴾
[النَّمل: 17]
﴿وحشر لسليمان جنوده من الجن والإنس والطير فهم يوزعون﴾ [النَّمل: 17]
Khaled Ibrahim Betala “Ndipo adasonkhanitsidwa kwa Sulaiman ankhondo ake ochokera m’ziwanda, anthu ndi mbalame, ndipo adawandandika m’magulumagulu |