×

M’mawa mwake iye anali kuyenda mu mzinda ndi mantha poyembekezera mavuto. Munthu 28:18 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Al-Qasas ⮕ (28:18) ayat 18 in Chichewa

28:18 Surah Al-Qasas ayat 18 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Al-Qasas ayat 18 - القَصَص - Page - Juz 20

﴿فَأَصۡبَحَ فِي ٱلۡمَدِينَةِ خَآئِفٗا يَتَرَقَّبُ فَإِذَا ٱلَّذِي ٱسۡتَنصَرَهُۥ بِٱلۡأَمۡسِ يَسۡتَصۡرِخُهُۥۚ قَالَ لَهُۥ مُوسَىٰٓ إِنَّكَ لَغَوِيّٞ مُّبِينٞ ﴾
[القَصَص: 18]

M’mawa mwake iye anali kuyenda mu mzinda ndi mantha poyembekezera mavuto. Munthu uja, amene amamuthandiza cha dzulo, adamuitananso kuti amuthandize. Mose adati, “Ndi choonekeratu kuti iwe ndiwe munthu wosokoneza.”

❮ Previous Next ❯

ترجمة: فأصبح في المدينة خائفا يترقب فإذا الذي استنصره بالأمس يستصرخه قال له, باللغة نيانجا

﴿فأصبح في المدينة خائفا يترقب فإذا الذي استنصره بالأمس يستصرخه قال له﴾ [القَصَص: 18]

Khaled Ibrahim Betala
“Choncho kudamuchera mu mzindamo (m’mawa mwake) uku ali wodzazidwa ndi mantha akuyembekezera (kuti chiyani chimpeze pa zimene zidachitika); pompo munthu uja adampempha dzulo chithandizo ankamuitana (kuti amthandize kumenyana ndi m’dani wake wina). Mûsa adamuuza: “Ndithudi ndiwe wopotoka owonekera.”
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek