Quran with Chichewa translation - Surah Al-Qasas ayat 26 - القَصَص - Page - Juz 20
﴿قَالَتۡ إِحۡدَىٰهُمَا يَٰٓأَبَتِ ٱسۡتَـٔۡجِرۡهُۖ إِنَّ خَيۡرَ مَنِ ٱسۡتَـٔۡجَرۡتَ ٱلۡقَوِيُّ ٱلۡأَمِينُ ﴾
[القَصَص: 26]
﴿قالت إحداهما ياأبت استأجره إن خير من استأجرت القوي الأمين﴾ [القَصَص: 26]
Khaled Ibrahim Betala “Mmodzi wa iwo (asungwana aja) adanena: “E bambo wanga mulembeni ntchito (kuti akhale woweta ziweto m’malo mwa ife). Ndithu amene alibwino kuti mumulembe ntchito ndi yemwe ali wamphamvu wokhulupirika (zonse ziwiri mwa iyeyu zirimo) |