×

Atate adati, “Ine ndidzakupatsa mmodzi wa ana anga aakazi kuti umukwatire ngati 28:27 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Al-Qasas ⮕ (28:27) ayat 27 in Chichewa

28:27 Surah Al-Qasas ayat 27 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Al-Qasas ayat 27 - القَصَص - Page - Juz 20

﴿قَالَ إِنِّيٓ أُرِيدُ أَنۡ أُنكِحَكَ إِحۡدَى ٱبۡنَتَيَّ هَٰتَيۡنِ عَلَىٰٓ أَن تَأۡجُرَنِي ثَمَٰنِيَ حِجَجٖۖ فَإِنۡ أَتۡمَمۡتَ عَشۡرٗا فَمِنۡ عِندِكَۖ وَمَآ أُرِيدُ أَنۡ أَشُقَّ عَلَيۡكَۚ سَتَجِدُنِيٓ إِن شَآءَ ٱللَّهُ مِنَ ٱلصَّٰلِحِينَ ﴾
[القَصَص: 27]

Atate adati, “Ine ndidzakupatsa mmodzi wa ana anga aakazi kuti umukwatire ngati ungakhale zaka zisanu ndi zitatu uli kundigwirira ntchito. Koma ngati ufuna ukhoza kugwira ntchito zaka khumi. Ine sindifuna kukuzunza ayi. Ngati Mulungu afuna, udzaona kuti ine ndine munthu wangwiro.”

❮ Previous Next ❯

ترجمة: قال إني أريد أن أنكحك إحدى ابنتي هاتين على أن تأجرني ثماني, باللغة نيانجا

﴿قال إني أريد أن أنكحك إحدى ابنتي هاتين على أن تأجرني ثماني﴾ [القَصَص: 27]

Khaled Ibrahim Betala
“(Shuaib) adati (kwa iye): “Ine ndikufuna kukukwatitsa mmodzi mwa asungwana anga awiriwa, chiongo chake ndikundigwilira ntchito zaka zisanu ndi zitatu; ngati utakwaniritsa zaka khumi ndiye kuti nkufuna kwako. Sindikufuna kukuvutitsa (pokuchulukitsira zaka); undipeza, Allah akafuna, kuti ndine mmodzi wa anthu abwino, (wokwaniritsa lonjezo).”
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek