Quran with Chichewa translation - Surah Al-Qasas ayat 28 - القَصَص - Page - Juz 20
﴿قَالَ ذَٰلِكَ بَيۡنِي وَبَيۡنَكَۖ أَيَّمَا ٱلۡأَجَلَيۡنِ قَضَيۡتُ فَلَا عُدۡوَٰنَ عَلَيَّۖ وَٱللَّهُ عَلَىٰ مَا نَقُولُ وَكِيلٞ ﴾
[القَصَص: 28]
﴿قال ذلك بيني وبينك أيما الأجلين قضيت فلا عدوان علي والله على﴾ [القَصَص: 28]
Khaled Ibrahim Betala “(Mûsa) adati: “Zimene mwandilonjezazi zili pakati pa ine ndi inu. Nyengo iriyonse imene ndikwaniritse pa ziwirizi (pogwira ntchitoyo, ndiye kuti ndakwaniritsa lonjezo lanu) musandichitire mtopola. Ndipo Allah ndiye Muyang’aniri pa zomwe tikukambazi.” |