×

Ndipo pamene adamaliza nthawi yake, iye anali kupita ndi mkazi wake. Mose 28:29 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Al-Qasas ⮕ (28:29) ayat 29 in Chichewa

28:29 Surah Al-Qasas ayat 29 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Al-Qasas ayat 29 - القَصَص - Page - Juz 20

﴿۞ فَلَمَّا قَضَىٰ مُوسَى ٱلۡأَجَلَ وَسَارَ بِأَهۡلِهِۦٓ ءَانَسَ مِن جَانِبِ ٱلطُّورِ نَارٗاۖ قَالَ لِأَهۡلِهِ ٱمۡكُثُوٓاْ إِنِّيٓ ءَانَسۡتُ نَارٗا لَّعَلِّيٓ ءَاتِيكُم مِّنۡهَا بِخَبَرٍ أَوۡ جَذۡوَةٖ مِّنَ ٱلنَّارِ لَعَلَّكُمۡ تَصۡطَلُونَ ﴾
[القَصَص: 29]

Ndipo pamene adamaliza nthawi yake, iye anali kupita ndi mkazi wake. Mose adaona moto kuonjezera pa phiri la Sinai. Iye adati kwa mkazi wake, “Khala pano chifukwa ndili kuona moto. Mwina mwake ndikhoza kubweretsa kuchokera kumeneko nkhani kapena mwatso woyaka umene ukhoza kuotha.”

❮ Previous Next ❯

ترجمة: فلما قضى موسى الأجل وسار بأهله آنس من جانب الطور نارا قال, باللغة نيانجا

﴿فلما قضى موسى الأجل وسار بأهله آنس من جانب الطور نارا قال﴾ [القَصَص: 29]

Khaled Ibrahim Betala
“Mûsa pamene adakwaniritsa nyengoyo, adanyamuka ndi banja lake (kubwerera kwao) adaona moto kumbali ya phiri. Adauza banja lake: “Dikirani ndithudi ine ndaona moto mwina mwake ndingakutengereni nkhani za kumeneko kapena chikuni cha moto kuti muothe.”
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek