×

Ndipo pamene Mose adadza kwa iwo ndi zizindikiro zathu zooneka, iwo adati, 28:36 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Al-Qasas ⮕ (28:36) ayat 36 in Chichewa

28:36 Surah Al-Qasas ayat 36 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Al-Qasas ayat 36 - القَصَص - Page - Juz 20

﴿فَلَمَّا جَآءَهُم مُّوسَىٰ بِـَٔايَٰتِنَا بَيِّنَٰتٖ قَالُواْ مَا هَٰذَآ إِلَّا سِحۡرٞ مُّفۡتَرٗى وَمَا سَمِعۡنَا بِهَٰذَا فِيٓ ءَابَآئِنَا ٱلۡأَوَّلِينَ ﴾
[القَصَص: 36]

Ndipo pamene Mose adadza kwa iwo ndi zizindikiro zathu zooneka, iwo adati, “Izi si zina ayi koma matsenga ongopeka ndiponso ife sitidamvepo kuti za mtundu uwu zinachitikapo kuchokera kwa makolo athu akale.”

❮ Previous Next ❯

ترجمة: فلما جاءهم موسى بآياتنا بينات قالوا ما هذا إلا سحر مفترى وما, باللغة نيانجا

﴿فلما جاءهم موسى بآياتنا بينات قالوا ما هذا إلا سحر مفترى وما﴾ [القَصَص: 36]

Khaled Ibrahim Betala
“Pamene Mûsa adawadzera ndi zizindikiro zathu zoonekera poyera, adati: “Ichi sichina koma ndi matsenga wopeka; sitidamvepo zimenezi kumakolo athu akale.”
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek