×

Farawo ndi Asirikali ake adadzikweza kwambiri mu dziko la Aiguputo popanda chifukwa 28:39 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Al-Qasas ⮕ (28:39) ayat 39 in Chichewa

28:39 Surah Al-Qasas ayat 39 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Al-Qasas ayat 39 - القَصَص - Page - Juz 20

﴿وَٱسۡتَكۡبَرَ هُوَ وَجُنُودُهُۥ فِي ٱلۡأَرۡضِ بِغَيۡرِ ٱلۡحَقِّ وَظَنُّوٓاْ أَنَّهُمۡ إِلَيۡنَا لَا يُرۡجَعُونَ ﴾
[القَصَص: 39]

Farawo ndi Asirikali ake adadzikweza kwambiri mu dziko la Aiguputo popanda chifukwa ndipo iwo anali kuganiza kuti sadzabwereranso kwa Ife

❮ Previous Next ❯

ترجمة: واستكبر هو وجنوده في الأرض بغير الحق وظنوا أنهم إلينا لا يرجعون, باللغة نيانجا

﴿واستكبر هو وجنوده في الأرض بغير الحق وظنوا أنهم إلينا لا يرجعون﴾ [القَصَص: 39]

Khaled Ibrahim Betala
“Ndipo iye pamodzi ndi makamu ake ankhondo adadzitukumula pa dziko popanda chilungamo ndipo ankaganiza kuti iwo sadzabwelere kwa Ife
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek