Quran with Chichewa translation - Surah Al-Qasas ayat 51 - القَصَص - Page - Juz 20
﴿۞ وَلَقَدۡ وَصَّلۡنَا لَهُمُ ٱلۡقَوۡلَ لَعَلَّهُمۡ يَتَذَكَّرُونَ ﴾
[القَصَص: 51]
﴿ولقد وصلنا لهم القول لعلهم يتذكرون﴾ [القَصَص: 51]
Khaled Ibrahim Betala “Ndipo ndithu tafikitsa mawu kwa iwo mochulukitsa, mwatsatanetsatane kuti iwo akumbukire |