×

Zinthu zimene mwapatsidwa si zina koma chakudya ndiponso chionetsero chopanda pake cha 28:60 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Al-Qasas ⮕ (28:60) ayat 60 in Chichewa

28:60 Surah Al-Qasas ayat 60 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Al-Qasas ayat 60 - القَصَص - Page - Juz 20

﴿وَمَآ أُوتِيتُم مِّن شَيۡءٖ فَمَتَٰعُ ٱلۡحَيَوٰةِ ٱلدُّنۡيَا وَزِينَتُهَاۚ وَمَا عِندَ ٱللَّهِ خَيۡرٞ وَأَبۡقَىٰٓۚ أَفَلَا تَعۡقِلُونَ ﴾
[القَصَص: 60]

Zinthu zimene mwapatsidwa si zina koma chakudya ndiponso chionetsero chopanda pake cha m’moyo uno. Koma chimene chili ndi Mulungu ndicho chabwino ndiponso chokhalitsa. Kodi simungathe kuzindikira

❮ Previous Next ❯

ترجمة: وما أوتيتم من شيء فمتاع الحياة الدنيا وزينتها وما عند الله خير, باللغة نيانجا

﴿وما أوتيتم من شيء فمتاع الحياة الدنيا وزينتها وما عند الله خير﴾ [القَصَص: 60]

Khaled Ibrahim Betala
“Ndipo chilichonse chimene mwapatsidwa nchosangalatsa cha moyo wa pa dziko, ndiponso chokometsera chake (chomwe sichikhalira kutha); koma chomwe chili kwa Allah ndicho chabwino, chamuyaya; kodi bwanji simukuzindikira
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek