×

Kunena za m’moyo umene uli nkudza, udzakhala wa iwo amene sadzikweza pa 28:83 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Al-Qasas ⮕ (28:83) ayat 83 in Chichewa

28:83 Surah Al-Qasas ayat 83 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Al-Qasas ayat 83 - القَصَص - Page - Juz 20

﴿تِلۡكَ ٱلدَّارُ ٱلۡأٓخِرَةُ نَجۡعَلُهَا لِلَّذِينَ لَا يُرِيدُونَ عُلُوّٗا فِي ٱلۡأَرۡضِ وَلَا فَسَادٗاۚ وَٱلۡعَٰقِبَةُ لِلۡمُتَّقِينَ ﴾
[القَصَص: 83]

Kunena za m’moyo umene uli nkudza, udzakhala wa iwo amene sadzikweza pa dziko lapansi kapena kuchita zoipa. Ndipo mapeto abwino ndi a iwo amene ali angwiro

❮ Previous Next ❯

ترجمة: تلك الدار الآخرة نجعلها للذين لا يريدون علوا في الأرض ولا فسادا, باللغة نيانجا

﴿تلك الدار الآخرة نجعلها للذين لا يريدون علوا في الأرض ولا فسادا﴾ [القَصَص: 83]

Khaled Ibrahim Betala
“Nyumba yomalizirayo tikawapangira amene sakufuna kudzikweza pa dziko ndi kuononga. Ndipo malekezero abwino adzakhala a wanthu owopa (Allah)
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek