×

Aliyense amene achita zabwino adzalipidwa zochuluka. Koma iye amene achita zoipa ndiponso 28:84 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Al-Qasas ⮕ (28:84) ayat 84 in Chichewa

28:84 Surah Al-Qasas ayat 84 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Al-Qasas ayat 84 - القَصَص - Page - Juz 20

﴿مَن جَآءَ بِٱلۡحَسَنَةِ فَلَهُۥ خَيۡرٞ مِّنۡهَاۖ وَمَن جَآءَ بِٱلسَّيِّئَةِ فَلَا يُجۡزَى ٱلَّذِينَ عَمِلُواْ ٱلسَّيِّـَٔاتِ إِلَّا مَا كَانُواْ يَعۡمَلُونَ ﴾
[القَصَص: 84]

Aliyense amene achita zabwino adzalipidwa zochuluka. Koma iye amene achita zoipa ndiponso iwo amene achita ntchito zoipa adzangolipidwa molingana ndi zimene anali kuchita

❮ Previous Next ❯

ترجمة: من جاء بالحسنة فله خير منها ومن جاء بالسيئة فلا يجزى الذين, باللغة نيانجا

﴿من جاء بالحسنة فله خير منها ومن جاء بالسيئة فلا يجزى الذين﴾ [القَصَص: 84]

Khaled Ibrahim Betala
“Amene achite chabwino, adzapeza mphoto yoposa chimene adachitacho ndipo amene achite choipa sadzalipidwa (china chake) koma zoipa zomwezo zimene adali kuzichita
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek