×

Chifukwa inu mumapembedza mafano oonjezera pa Mulungu ndipo inu mumapeka bodza. Zinthu 29:17 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Al-‘Ankabut ⮕ (29:17) ayat 17 in Chichewa

29:17 Surah Al-‘Ankabut ayat 17 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Al-‘Ankabut ayat 17 - العَنكبُوت - Page - Juz 20

﴿إِنَّمَا تَعۡبُدُونَ مِن دُونِ ٱللَّهِ أَوۡثَٰنٗا وَتَخۡلُقُونَ إِفۡكًاۚ إِنَّ ٱلَّذِينَ تَعۡبُدُونَ مِن دُونِ ٱللَّهِ لَا يَمۡلِكُونَ لَكُمۡ رِزۡقٗا فَٱبۡتَغُواْ عِندَ ٱللَّهِ ٱلرِّزۡقَ وَٱعۡبُدُوهُ وَٱشۡكُرُواْ لَهُۥٓۖ إِلَيۡهِ تُرۡجَعُونَ ﴾
[العَنكبُوت: 17]

Chifukwa inu mumapembedza mafano oonjezera pa Mulungu ndipo inu mumapeka bodza. Zinthu zimene mumapembedza zoonjezera pa Mulungu zilibemphamvuzokupatsanizofunazanu.Koteropemphani zofuna zanu kwa Mulungu ndipo muzimuthokoza Iye. Kwa Iye ndiko kumene mudzabwerera

❮ Previous Next ❯

ترجمة: إنما تعبدون من دون الله أوثانا وتخلقون إفكا إن الذين تعبدون من, باللغة نيانجا

﴿إنما تعبدون من دون الله أوثانا وتخلقون إفكا إن الذين تعبدون من﴾ [العَنكبُوت: 17]

Khaled Ibrahim Betala
“Ndithu inu mukupembedza mafano kusiya (kupembedza) Allah ndipo mwadzipangira chonama. Ndithu amene mukuwapembedzawo kusiya Allah, sangakupatseni rizq (madalitso) choncho funani rizq (madalitso) kwa Allah, ndipo mpembedzeni Iye Yekha ndi kumthokoza. Kwa Iye ndikomwe mudzabwerera (tsiku la chimaliziro)
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek