Quran with Chichewa translation - Surah Al-‘Ankabut ayat 18 - العَنكبُوت - Page - Juz 20
﴿وَإِن تُكَذِّبُواْ فَقَدۡ كَذَّبَ أُمَمٞ مِّن قَبۡلِكُمۡۖ وَمَا عَلَى ٱلرَّسُولِ إِلَّا ٱلۡبَلَٰغُ ٱلۡمُبِينُ ﴾
[العَنكبُوت: 18]
﴿وإن تكذبوا فقد كذب أمم من قبلكم وما على الرسول إلا البلاغ﴾ [العَنكبُوت: 18]
Khaled Ibrahim Betala “Ndipo ngati mutsutsa, ndithu mibadwo ya omwe adalipo patsogolo panu idatsutsanso. Ndipo kwa Mtumiki kulibe udindo wina koma kufikitsa uthenga woonekera poyera, (womveka bwino) |