×

onse amene amakana zizindikiro za Mulungu ndiponso zokumana naye m’moyo umene uli 29:23 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Al-‘Ankabut ⮕ (29:23) ayat 23 in Chichewa

29:23 Surah Al-‘Ankabut ayat 23 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Al-‘Ankabut ayat 23 - العَنكبُوت - Page - Juz 20

﴿وَٱلَّذِينَ كَفَرُواْ بِـَٔايَٰتِ ٱللَّهِ وَلِقَآئِهِۦٓ أُوْلَٰٓئِكَ يَئِسُواْ مِن رَّحۡمَتِي وَأُوْلَٰٓئِكَ لَهُمۡ عَذَابٌ أَلِيمٞ ﴾
[العَنكبُوت: 23]

onse amene amakana zizindikiro za Mulungu ndiponso zokumana naye m’moyo umene uli nkudza ndiwo amene amakayika za chifundo changa. Ndipo iwo adzalandira chilango chowawa kwambiri

❮ Previous Next ❯

ترجمة: والذين كفروا بآيات الله ولقائه أولئك يئسوا من رحمتي وأولئك لهم عذاب, باللغة نيانجا

﴿والذين كفروا بآيات الله ولقائه أولئك يئسوا من رحمتي وأولئك لهم عذاب﴾ [العَنكبُوت: 23]

Khaled Ibrahim Betala
“Ndipo amene akana Ayah (ndime) za Allah ndi kukumana Naye amenewo ndiwo ataya mtima pa zakupeza chifundo Changa, ndipo iwowo ndiwo adzapeza chilango chowawa
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek