×

Ndithudi iwo amene sakhulupirira, chuma chawo ndiponso ana awo sadzatha kuwapulumutsa ku 3:10 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah al-‘Imran ⮕ (3:10) ayat 10 in Chichewa

3:10 Surah al-‘Imran ayat 10 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah al-‘Imran ayat 10 - آل عِمران - Page - Juz 3

﴿إِنَّ ٱلَّذِينَ كَفَرُواْ لَن تُغۡنِيَ عَنۡهُمۡ أَمۡوَٰلُهُمۡ وَلَآ أَوۡلَٰدُهُم مِّنَ ٱللَّهِ شَيۡـٔٗاۖ وَأُوْلَٰٓئِكَ هُمۡ وَقُودُ ٱلنَّارِ ﴾
[آل عِمران: 10]

Ndithudi iwo amene sakhulupirira, chuma chawo ndiponso ana awo sadzatha kuwapulumutsa ku mkwiyo wa Mulungu ndipo iwo adzakhala nkhuni za ku Gahena

❮ Previous Next ❯

ترجمة: إن الذين كفروا لن تغني عنهم أموالهم ولا أولادهم من الله شيئا, باللغة نيانجا

﴿إن الذين كفروا لن تغني عنهم أموالهم ولا أولادهم من الله شيئا﴾ [آل عِمران: 10]

Khaled Ibrahim Betala
“Ndithu amene sadakhulupirire, chuma chawo sichidzawathandiza chilichonse ngakhalenso ana awo, ku chilango cha Allah. Ndipo iwo ndi nkhuni za ku Moto
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek