×

Ndi iwo amene, ngatiachitachigololokapenaalakwiramizimuyawo, amakumbukira Mulungu ndi kupempha chikhululukiro cha machimo awo, 3:135 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah al-‘Imran ⮕ (3:135) ayat 135 in Chichewa

3:135 Surah al-‘Imran ayat 135 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah al-‘Imran ayat 135 - آل عِمران - Page - Juz 4

﴿وَٱلَّذِينَ إِذَا فَعَلُواْ فَٰحِشَةً أَوۡ ظَلَمُوٓاْ أَنفُسَهُمۡ ذَكَرُواْ ٱللَّهَ فَٱسۡتَغۡفَرُواْ لِذُنُوبِهِمۡ وَمَن يَغۡفِرُ ٱلذُّنُوبَ إِلَّا ٱللَّهُ وَلَمۡ يُصِرُّواْ عَلَىٰ مَا فَعَلُواْ وَهُمۡ يَعۡلَمُونَ ﴾
[آل عِمران: 135]

Ndi iwo amene, ngatiachitachigololokapenaalakwiramizimuyawo, amakumbukira Mulungu ndi kupempha chikhululukiro cha machimo awo, ndipo palibe wina amene angakhululukire machimo kupatula Mulungu, ndipo sapitiliza kuchita zoipa pamene iwo ali nkudziwa

❮ Previous Next ❯

ترجمة: والذين إذا فعلوا فاحشة أو ظلموا أنفسهم ذكروا الله فاستغفروا لذنوبهم ومن, باللغة نيانجا

﴿والذين إذا فعلوا فاحشة أو ظلموا أنفسهم ذكروا الله فاستغفروا لذنوبهم ومن﴾ [آل عِمران: 135]

Khaled Ibrahim Betala
“Ndi amene amati akachita uve (wamachimo), kapena kudzichitira okha zoipa, amakumbukira Allah nampempha chikhululuko pa machimo awo. Kodi ndindani angakhululuke machimo kupatula Allah; ndipo napanda kupitiriza machimo omwe achita uku akudziwa
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek