×

“Ambuye wathu! Tipatseni ife zimene mudatilonjeza kudzera mwa Atumwi anu ndipo musadzatichititse 3:194 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah al-‘Imran ⮕ (3:194) ayat 194 in Chichewa

3:194 Surah al-‘Imran ayat 194 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah al-‘Imran ayat 194 - آل عِمران - Page - Juz 4

﴿رَبَّنَا وَءَاتِنَا مَا وَعَدتَّنَا عَلَىٰ رُسُلِكَ وَلَا تُخۡزِنَا يَوۡمَ ٱلۡقِيَٰمَةِۖ إِنَّكَ لَا تُخۡلِفُ ٱلۡمِيعَادَ ﴾
[آل عِمران: 194]

“Ambuye wathu! Tipatseni ife zimene mudatilonjeza kudzera mwa Atumwi anu ndipo musadzatichititse manyazi ife pa tsiku la kuuka kwa akufa chifukwa Inu simuphwanya lonjezo.”

❮ Previous Next ❯

ترجمة: ربنا وآتنا ما وعدتنا على رسلك ولا تخزنا يوم القيامة إنك لا, باللغة نيانجا

﴿ربنا وآتنا ما وعدتنا على رسلك ولا تخزنا يوم القيامة إنك لا﴾ [آل عِمران: 194]

Khaled Ibrahim Betala
““E, Mbuye wathu! Tipatseni zimene mudatilonjeza kupyolera mwa atumiki anu ndipo musadzatisambule tsiku lachimaliziro. Ndithudi, inu simuswa lonjezo.”
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek