×

“Ndithudi! Mulungu ndi Ambuye wanga ndi Ambuye wanu; ‘Motero m’pembedzeni Iye yekha.’ 3:51 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah al-‘Imran ⮕ (3:51) ayat 51 in Chichewa

3:51 Surah al-‘Imran ayat 51 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah al-‘Imran ayat 51 - آل عِمران - Page - Juz 3

﴿إِنَّ ٱللَّهَ رَبِّي وَرَبُّكُمۡ فَٱعۡبُدُوهُۚ هَٰذَا صِرَٰطٞ مُّسۡتَقِيمٞ ﴾
[آل عِمران: 51]

“Ndithudi! Mulungu ndi Ambuye wanga ndi Ambuye wanu; ‘Motero m’pembedzeni Iye yekha.’ Imeneyi ndiyo njira yoyenera.”

❮ Previous Next ❯

ترجمة: إن الله ربي وربكم فاعبدوه هذا صراط مستقيم, باللغة نيانجا

﴿إن الله ربي وربكم فاعبدوه هذا صراط مستقيم﴾ [آل عِمران: 51]

Khaled Ibrahim Betala
““Ndithu Allah ndiye Mbuye wanga ndiponso Mbuye wanu; choncho mupembedzeni. Iyi ndiyo njira yoongoka.”
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek