×

Kodiinundinuamenemumatsutsana pa nkhani zimene mumazidziwa? Nanga ndi chifukwa chiyani mukutsutsana pa zinthu 3:66 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah al-‘Imran ⮕ (3:66) ayat 66 in Chichewa

3:66 Surah al-‘Imran ayat 66 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah al-‘Imran ayat 66 - آل عِمران - Page - Juz 3

﴿هَٰٓأَنتُمۡ هَٰٓؤُلَآءِ حَٰجَجۡتُمۡ فِيمَا لَكُم بِهِۦ عِلۡمٞ فَلِمَ تُحَآجُّونَ فِيمَا لَيۡسَ لَكُم بِهِۦ عِلۡمٞۚ وَٱللَّهُ يَعۡلَمُ وَأَنتُمۡ لَا تَعۡلَمُونَ ﴾
[آل عِمران: 66]

Kodiinundinuamenemumatsutsana pa nkhani zimene mumazidziwa? Nanga ndi chifukwa chiyani mukutsutsana pa zinthu zimene simudziwa? Ndi Mulungu amene amadziwa ndipo inu simuzidziwa

❮ Previous Next ❯

ترجمة: ها أنتم هؤلاء حاججتم فيما لكم به علم فلم تحاجون فيما ليس, باللغة نيانجا

﴿ها أنتم هؤلاء حاججتم فيما لكم به علم فلم تحاجون فيما ليس﴾ [آل عِمران: 66]

Khaled Ibrahim Betala
“Taonani! Inu mudatsutsana pa zomwe mudazidziwa, nanga bwanji mukutsutsana pa zomwe simuzidziwa? Allah ndi Yemwe akudziwa. Pomwe inu simudziwa
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek