×

Inde, aliyense amene amakwaniritsa lonjezo lake ndi kuopa Mulungu kwambiri, ndithudi Mulungu 3:76 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah al-‘Imran ⮕ (3:76) ayat 76 in Chichewa

3:76 Surah al-‘Imran ayat 76 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah al-‘Imran ayat 76 - آل عِمران - Page - Juz 3

﴿بَلَىٰۚ مَنۡ أَوۡفَىٰ بِعَهۡدِهِۦ وَٱتَّقَىٰ فَإِنَّ ٱللَّهَ يُحِبُّ ٱلۡمُتَّقِينَ ﴾
[آل عِمران: 76]

Inde, aliyense amene amakwaniritsa lonjezo lake ndi kuopa Mulungu kwambiri, ndithudi Mulungu amakonda iwo amene amamuopa Iye

❮ Previous Next ❯

ترجمة: بلى من أوفى بعهده واتقى فإن الله يحب المتقين, باللغة نيانجا

﴿بلى من أوفى بعهده واتقى فإن الله يحب المتقين﴾ [آل عِمران: 76]

Khaled Ibrahim Betala
“Sichoncho (monga momwe akunenera)! Koma amene akukwaniritsa lonjezo lake napewa machimo (ndiyemwe ayenera kukhala wokondedwa kwa Allah). Ndithudi, Allah amakonda opewa machimo
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek