Quran with Chichewa translation - Surah al-‘Imran ayat 83 - آل عِمران - Page - Juz 3
﴿أَفَغَيۡرَ دِينِ ٱللَّهِ يَبۡغُونَ وَلَهُۥٓ أَسۡلَمَ مَن فِي ٱلسَّمَٰوَٰتِ وَٱلۡأَرۡضِ طَوۡعٗا وَكَرۡهٗا وَإِلَيۡهِ يُرۡجَعُونَ ﴾
[آل عِمران: 83]
﴿أفغير دين الله يبغون وله أسلم من في السموات والأرض طوعا وكرها﴾ [آل عِمران: 83]
Khaled Ibrahim Betala “Kodi akufuna chipembedzo chomwe si cha Allah pomwe chinthu chilichonse chili kumwamba ndi pansi chikugonjera Iye, mofuna kapena mosafuna? Ndipo onse adzabwezedwa kwa Iye |