×

Ndithudi iwo amene adakana atayamba akhulupirira ndipo anapitiliza kusakhulupilira kwawo, kulapa kwawo 3:90 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah al-‘Imran ⮕ (3:90) ayat 90 in Chichewa

3:90 Surah al-‘Imran ayat 90 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah al-‘Imran ayat 90 - آل عِمران - Page - Juz 3

﴿إِنَّ ٱلَّذِينَ كَفَرُواْ بَعۡدَ إِيمَٰنِهِمۡ ثُمَّ ٱزۡدَادُواْ كُفۡرٗا لَّن تُقۡبَلَ تَوۡبَتُهُمۡ وَأُوْلَٰٓئِكَ هُمُ ٱلضَّآلُّونَ ﴾
[آل عِمران: 90]

Ndithudi iwo amene adakana atayamba akhulupirira ndipo anapitiliza kusakhulupilira kwawo, kulapa kwawo sikudzavomerezeka. Ndipo iwo ndi osochera

❮ Previous Next ❯

ترجمة: إن الذين كفروا بعد إيمانهم ثم ازدادوا كفرا لن تقبل توبتهم وأولئك, باللغة نيانجا

﴿إن الذين كفروا بعد إيمانهم ثم ازدادوا كفرا لن تقبل توبتهم وأولئك﴾ [آل عِمران: 90]

Khaled Ibrahim Betala
“Ndithudi, amene atuluka m’chikhulupiliro pambuyo pokhulupirira, kenako naonjezera kusakhulupirira, kulapa kwawo sikudzavomerezedwa konse. Ndipo iwo ndiosekera
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek