Quran with Chichewa translation - Surah Ar-Rum ayat 17 - الرُّوم - Page - Juz 21
﴿فَسُبۡحَٰنَ ٱللَّهِ حِينَ تُمۡسُونَ وَحِينَ تُصۡبِحُونَ ﴾
[الرُّوم: 17]
﴿فسبحان الله حين تمسون وحين تصبحون﴾ [الرُّوم: 17]
Khaled Ibrahim Betala “Choncho, lemekezani Allah pamene mukulowa m’nthawi za usiku (popemphera Magrbi ndi Isha); ndi pamene mukulowa m’nthawi ya m’bandakucha (popemphera pemphero la Fajr) |