Quran with Chichewa translation - Surah Ar-Rum ayat 18 - الرُّوم - Page - Juz 21
﴿وَلَهُ ٱلۡحَمۡدُ فِي ٱلسَّمَٰوَٰتِ وَٱلۡأَرۡضِ وَعَشِيّٗا وَحِينَ تُظۡهِرُونَ ﴾
[الرُّوم: 18]
﴿وله الحمد في السموات والأرض وعشيا وحين تظهرون﴾ [الرُّوم: 18]
Khaled Ibrahim Betala “Kutamandidwa konse, kumwamba ndi pansi nkwa Allah. Ndipo (mulemekezeni) m’nthawi ya madzulo (popemphera Asr) ndi pomwe mukulowa m’nthawi yamasana (Dhuhr) |