Quran with Chichewa translation - Surah Luqman ayat 17 - لُقمَان - Page - Juz 21
﴿يَٰبُنَيَّ أَقِمِ ٱلصَّلَوٰةَ وَأۡمُرۡ بِٱلۡمَعۡرُوفِ وَٱنۡهَ عَنِ ٱلۡمُنكَرِ وَٱصۡبِرۡ عَلَىٰ مَآ أَصَابَكَۖ إِنَّ ذَٰلِكَ مِنۡ عَزۡمِ ٱلۡأُمُورِ ﴾
[لُقمَان: 17]
﴿يابني أقم الصلاة وأمر بالمعروف وانه عن المنكر واصبر على ما أصابك﴾ [لُقمَان: 17]
Khaled Ibrahim Betala ““E iwe mwana wanga! Pemphera Swala moyenera, lamula zabwino, letsa zoipa, ndipo pirira ndi masautso amene akukhudza. Ndithu zimenezo ndizinthu zofunika kuziikirapo mtima (munthu aliyense).” |