×

Aliyense amene adzipereka kwa Mulungu ndipo amachita ntchito zabwino, amagwiritsa chotsekulira chimene 31:22 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Luqman ⮕ (31:22) ayat 22 in Chichewa

31:22 Surah Luqman ayat 22 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Luqman ayat 22 - لُقمَان - Page - Juz 21

﴿۞ وَمَن يُسۡلِمۡ وَجۡهَهُۥٓ إِلَى ٱللَّهِ وَهُوَ مُحۡسِنٞ فَقَدِ ٱسۡتَمۡسَكَ بِٱلۡعُرۡوَةِ ٱلۡوُثۡقَىٰۗ وَإِلَى ٱللَّهِ عَٰقِبَةُ ٱلۡأُمُورِ ﴾
[لُقمَان: 22]

Aliyense amene adzipereka kwa Mulungu ndipo amachita ntchito zabwino, amagwiritsa chotsekulira chimene chiyenera kugwiridwa ndipo kwa Mulungu zinthu zonse zidzabwerera

❮ Previous Next ❯

ترجمة: ومن يسلم وجهه إلى الله وهو محسن فقد استمسك بالعروة الوثقى وإلى, باللغة نيانجا

﴿ومن يسلم وجهه إلى الله وهو محسن فقد استمسك بالعروة الوثقى وإلى﴾ [لُقمَان: 22]

Khaled Ibrahim Betala
“Ndipo amene akupereka nkhope yake kwa Allah (amene akugonjera Allah kwatunthu) ali ochita zabwino, ndiye kuti wagwira chogwilira cholimba. Ndipo mapeto a zinthu zonse nkwa Allah basi
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek