×

Iwo amene amakhulupirira ndipo amachita ntchito zabwino, adzalandira minda ngati malo awo 32:19 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah As-Sajdah ⮕ (32:19) ayat 19 in Chichewa

32:19 Surah As-Sajdah ayat 19 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah As-Sajdah ayat 19 - السَّجدة - Page - Juz 21

﴿أَمَّا ٱلَّذِينَ ءَامَنُواْ وَعَمِلُواْ ٱلصَّٰلِحَٰتِ فَلَهُمۡ جَنَّٰتُ ٱلۡمَأۡوَىٰ نُزُلَۢا بِمَا كَانُواْ يَعۡمَلُونَ ﴾
[السَّجدة: 19]

Iwo amene amakhulupirira ndipo amachita ntchito zabwino, adzalandira minda ngati malo awo okhala chifukwa cha ntchito zawo zabwino zimene anachita

❮ Previous Next ❯

ترجمة: أما الذين آمنوا وعملوا الصالحات فلهم جنات المأوى نـزلا بما كانوا يعملون, باللغة نيانجا

﴿أما الذين آمنوا وعملوا الصالحات فلهم جنات المأوى نـزلا بما كانوا يعملون﴾ [السَّجدة: 19]

Khaled Ibrahim Betala
“Tsono amene akhulupirira ndi kumachita zabwino, adzalandira Minda yokhalamo yokongola, monga phwando lawo pa zimene ankachita
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek