Quran with Chichewa translation - Surah As-Sajdah ayat 28 - السَّجدة - Page - Juz 21
﴿وَيَقُولُونَ مَتَىٰ هَٰذَا ٱلۡفَتۡحُ إِن كُنتُمۡ صَٰدِقِينَ ﴾
[السَّجدة: 28]
﴿ويقولون متى هذا الفتح إن كنتم صادقين﴾ [السَّجدة: 28]
Khaled Ibrahim Betala “Ndipo akunena: “Kulamulidwa kumeneku (kwa tsiku la chimaliziro) kudzachitika liti, ngati mukunenadi zoona?” |