×

Nena, “Pa tsiku lachiweruzo, chikhulupiriro cha iwo amene sakhulupirira sichidzawathandiza ndiponso sadzapeza 32:29 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah As-Sajdah ⮕ (32:29) ayat 29 in Chichewa

32:29 Surah As-Sajdah ayat 29 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah As-Sajdah ayat 29 - السَّجدة - Page - Juz 21

﴿قُلۡ يَوۡمَ ٱلۡفَتۡحِ لَا يَنفَعُ ٱلَّذِينَ كَفَرُوٓاْ إِيمَٰنُهُمۡ وَلَا هُمۡ يُنظَرُونَ ﴾
[السَّجدة: 29]

Nena, “Pa tsiku lachiweruzo, chikhulupiriro cha iwo amene sakhulupirira sichidzawathandiza ndiponso sadzapeza mpumulo.”

❮ Previous Next ❯

ترجمة: قل يوم الفتح لا ينفع الذين كفروا إيمانهم ولا هم ينظرون, باللغة نيانجا

﴿قل يوم الفتح لا ينفع الذين كفروا إيمانهم ولا هم ينظرون﴾ [السَّجدة: 29]

Khaled Ibrahim Betala
“Nena: “Tsiku la chiweruzirolo, amene sadakhulupirire, chikhulupiriro chawo sichidzawathandiza. Ndipo sadzapatsidwa nthawi yoyembekezera (kuti mizimu yawo isachoke ayambe akhulupirira kaye, mngero wa imfa akadzawadzera).”
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek