×

Taona! Gulu lina limene lidali pakati pawo lidati, “Inu anthu a ku 33:13 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Al-Ahzab ⮕ (33:13) ayat 13 in Chichewa

33:13 Surah Al-Ahzab ayat 13 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Al-Ahzab ayat 13 - الأحزَاب - Page - Juz 21

﴿وَإِذۡ قَالَت طَّآئِفَةٞ مِّنۡهُمۡ يَٰٓأَهۡلَ يَثۡرِبَ لَا مُقَامَ لَكُمۡ فَٱرۡجِعُواْۚ وَيَسۡتَـٔۡذِنُ فَرِيقٞ مِّنۡهُمُ ٱلنَّبِيَّ يَقُولُونَ إِنَّ بُيُوتَنَا عَوۡرَةٞ وَمَا هِيَ بِعَوۡرَةٍۖ إِن يُرِيدُونَ إِلَّا فِرَارٗا ﴾
[الأحزَاب: 13]

Taona! Gulu lina limene lidali pakati pawo lidati, “Inu anthu a ku Yasrib simungawagonjetse awa ayi kotero bwererani m’mbuyo!” Ndipo kagulu kena kamapempha chilolezo kwa Mtumwi ndipo kadati, “Ndithudi nyumba zathu zilibe woziteteza.” Koma sizinali choncho ayi koma kuti iwo amangofuna kupeza njira yothawira

❮ Previous Next ❯

ترجمة: وإذ قالت طائفة منهم ياأهل يثرب لا مقام لكم فارجعوا ويستأذن فريق, باللغة نيانجا

﴿وإذ قالت طائفة منهم ياأهل يثرب لا مقام لكم فارجعوا ويستأذن فريق﴾ [الأحزَاب: 13]

Khaled Ibrahim Betala
“Ndipo pamene gulu lina mwa iwo lidanena: “E inu nzika za mu Yathiriba (Madina)! Palibe njira kwa inu yokhalira (pa nkhondo yogonjayi). Choncho bwererani (ku nyumba zanu; msiyeni Muhammad alimbane yekha ndi adani ake).” Ndipo gulu lina la nkhondo lochokera mwa iwo limapempha chilolezo kwa Mneneri (s.a.w) ( chobwelera ku Madina) ponena (kuti): “Ndithu nyumba zathu nzamaliseche (zopanda chitetezo).” Koma izo sizamaliseche. Sakufuna china, koma kuthawa basi
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek