Quran with Chichewa translation - Surah Al-Ahzab ayat 15 - الأحزَاب - Page - Juz 21
﴿وَلَقَدۡ كَانُواْ عَٰهَدُواْ ٱللَّهَ مِن قَبۡلُ لَا يُوَلُّونَ ٱلۡأَدۡبَٰرَۚ وَكَانَ عَهۡدُ ٱللَّهِ مَسۡـُٔولٗا ﴾
[الأحزَاب: 15]
﴿ولقد كانوا عاهدوا الله من قبل لا يولون الأدبار وكان عهد الله﴾ [الأحزَاب: 15]
Khaled Ibrahim Betala “Ndipo ndithu (awa amene adathawa pabwalo la nkhondo), adali atamulonjeza kale Allah (kuti iwo) sadzatembenuza misana (kuthawa). Ndipo lonjezo la Allah nlofunsidwa. (Choncho iwo adzafunsidwa pa zomwe adalonjeza kwa Allah) |