×

Kuti Mulungu akhoza kupereka malipiro kwa anthu olungama chifukwa cha chilungamo chawo 33:24 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Al-Ahzab ⮕ (33:24) ayat 24 in Chichewa

33:24 Surah Al-Ahzab ayat 24 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Al-Ahzab ayat 24 - الأحزَاب - Page - Juz 21

﴿لِّيَجۡزِيَ ٱللَّهُ ٱلصَّٰدِقِينَ بِصِدۡقِهِمۡ وَيُعَذِّبَ ٱلۡمُنَٰفِقِينَ إِن شَآءَ أَوۡ يَتُوبَ عَلَيۡهِمۡۚ إِنَّ ٱللَّهَ كَانَ غَفُورٗا رَّحِيمٗا ﴾
[الأحزَاب: 24]

Kuti Mulungu akhoza kupereka malipiro kwa anthu olungama chifukwa cha chilungamo chawo ndi kulanga anthu a chinyengo ngati chimenecho ndicho chifuniro chake kapena kuwakhululukira chifukwa Mulungu ndi wokhululukira ndi Mwini chisoni chosatha

❮ Previous Next ❯

ترجمة: ليجزي الله الصادقين بصدقهم ويعذب المنافقين إن شاء أو يتوب عليهم إن, باللغة نيانجا

﴿ليجزي الله الصادقين بصدقهم ويعذب المنافقين إن شاء أو يتوب عليهم إن﴾ [الأحزَاب: 24]

Khaled Ibrahim Betala
“Kuti Allah awalipire owona chifukwa cha kuona kwawo; ndi kuti awalange achiphamaso ngati atafuna, kapena kuwalandira kulapa kwawo (ngati atalapa). Ndithu Allah Ngokhululuka kwabasi Ngwachisoni chosatha
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek