Quran with Chichewa translation - Surah Saba’ ayat 11 - سَبإ - Page - Juz 22
﴿أَنِ ٱعۡمَلۡ سَٰبِغَٰتٖ وَقَدِّرۡ فِي ٱلسَّرۡدِۖ وَٱعۡمَلُواْ صَٰلِحًاۖ إِنِّي بِمَا تَعۡمَلُونَ بَصِيرٞ ﴾
[سَبإ: 11]
﴿أن اعمل سابغات وقدر في السرد واعملوا صالحا إني بما تعملون بصير﴾ [سَبإ: 11]
Khaled Ibrahim Betala “(Tidati kwa iye:) “Panga zovala (za chitsulo) zophanuka (zokwana thupi lonse, zodzitetezera pa nkhondo), ndipo linga bwino m’kulumikiza ndi poluka. Potero chitani zabwino. Ndithu Ine ndikuona zonse zimene mukuchita.” |