Quran with Chichewa translation - Surah Saba’ ayat 10 - سَبإ - Page - Juz 22
﴿۞ وَلَقَدۡ ءَاتَيۡنَا دَاوُۥدَ مِنَّا فَضۡلٗاۖ يَٰجِبَالُ أَوِّبِي مَعَهُۥ وَٱلطَّيۡرَۖ وَأَلَنَّا لَهُ ٱلۡحَدِيدَ ﴾
[سَبإ: 10]
﴿ولقد آتينا داود منا فضلا ياجبال أوبي معه والطير وألنا له الحديد﴾ [سَبإ: 10]
Khaled Ibrahim Betala “Ndithudi, Daud tidampatsa chisomo chachikulu chochokera kwa Ife. (Ndipo tidauza mapiri kuti akhale akuvomereza mapemphero a Daud pothandizana naye. Tidati): “E inu mapiri pamodzi ndi iye Daud, lemekezani (Allah), ndi inunso mbalame.” Ndipo tidamufewetsera chitsulo |