Quran with Chichewa translation - Surah Saba’ ayat 35 - سَبإ - Page - Juz 22
﴿وَقَالُواْ نَحۡنُ أَكۡثَرُ أَمۡوَٰلٗا وَأَوۡلَٰدٗا وَمَا نَحۡنُ بِمُعَذَّبِينَ ﴾
[سَبإ: 35]
﴿وقالوا نحن أكثر أموالا وأولادا وما نحن بمعذبين﴾ [سَبإ: 35]
Khaled Ibrahim Betala “Ndipo ankanena (monyada): “Ife tili ndi chuma chambiri ndi ana (amhiri); choncho ife sitidzalangidwa (pa tsiku la chimaliziro).” |