×

Ife sitidatumizepo Mchenjezi ku mzinda wina uliwonse umene anthu ake opeza bwino 34:34 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah Saba’ ⮕ (34:34) ayat 34 in Chichewa

34:34 Surah Saba’ ayat 34 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah Saba’ ayat 34 - سَبإ - Page - Juz 22

﴿وَمَآ أَرۡسَلۡنَا فِي قَرۡيَةٖ مِّن نَّذِيرٍ إِلَّا قَالَ مُتۡرَفُوهَآ إِنَّا بِمَآ أُرۡسِلۡتُم بِهِۦ كَٰفِرُونَ ﴾
[سَبإ: 34]

Ife sitidatumizepo Mchenjezi ku mzinda wina uliwonse umene anthu ake opeza bwino sadanenepo mawu oti, “Ndithudiifesitikhulupirirauthengaumenewatumizidwa.”

❮ Previous Next ❯

ترجمة: وما أرسلنا في قرية من نذير إلا قال مترفوها إنا بما أرسلتم, باللغة نيانجا

﴿وما أرسلنا في قرية من نذير إلا قال مترفوها إنا بما أرسلتم﴾ [سَبإ: 34]

Khaled Ibrahim Betala
“Palibe pamene tidatuma mchenjezi m’mudzi uliwonse koma opeza bwino a m’mudzimo ankanena: “Ndithu ife tikuzikana zimene mwatumidwa nazozi.”
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek