Quran with Chichewa translation - Surah FaTir ayat 2 - فَاطِر - Page - Juz 22
﴿مَّا يَفۡتَحِ ٱللَّهُ لِلنَّاسِ مِن رَّحۡمَةٖ فَلَا مُمۡسِكَ لَهَاۖ وَمَا يُمۡسِكۡ فَلَا مُرۡسِلَ لَهُۥ مِنۢ بَعۡدِهِۦۚ وَهُوَ ٱلۡعَزِيزُ ٱلۡحَكِيمُ ﴾
[فَاطِر: 2]
﴿ما يفتح الله للناس من رحمة فلا ممسك لها وما يمسك فلا﴾ [فَاطِر: 2]
Khaled Ibrahim Betala “Chifundo chimene Allah angatsekule kwa anthu, palibe amene angachitsekereze. Ndipo chimene angachiletse palibe amene angachipereke kupatula Iye. Ndipo Iye ndi Mwini mphamvu zoposa, Wanzeru zakuya |