×

Kuyamikidwa konse ndi kwa Mulungu, Namalenga wakumwamba ndi dziko lapansi, amene adalenga 35:1 Chichewa translation

Quran infoChichewaSurah FaTir ⮕ (35:1) ayat 1 in Chichewa

35:1 Surah FaTir ayat 1 in Chichewa (نيانجا)

Quran with Chichewa translation - Surah FaTir ayat 1 - فَاطِر - Page - Juz 22

﴿ٱلۡحَمۡدُ لِلَّهِ فَاطِرِ ٱلسَّمَٰوَٰتِ وَٱلۡأَرۡضِ جَاعِلِ ٱلۡمَلَٰٓئِكَةِ رُسُلًا أُوْلِيٓ أَجۡنِحَةٖ مَّثۡنَىٰ وَثُلَٰثَ وَرُبَٰعَۚ يَزِيدُ فِي ٱلۡخَلۡقِ مَا يَشَآءُۚ إِنَّ ٱللَّهَ عَلَىٰ كُلِّ شَيۡءٖ قَدِيرٞ ﴾
[فَاطِر: 1]

Kuyamikidwa konse ndi kwa Mulungu, Namalenga wakumwamba ndi dziko lapansi, amene adalenga angelo, atumwi ouluka, amapiko awiri, atatu ndi anayi. Iye amachulukitsa zolengedwa mwachifuniro chake. Ndithudi Mulungu ali ndi mphamvu pa chinthu china chilichonse

❮ Previous Next ❯

ترجمة: الحمد لله فاطر السموات والأرض جاعل الملائكة رسلا أولي أجنحة مثنى وثلاث, باللغة نيانجا

﴿الحمد لله فاطر السموات والأرض جاعل الملائكة رسلا أولي أجنحة مثنى وثلاث﴾ [فَاطِر: 1]

Khaled Ibrahim Betala
“Kuyamikidwa konse nkwa Allah (Yekha) Muumbi wa thambo ndi nthaka (popanda chofanizira), amene adachita angelo kukhala atumwi eni mapiko, awiriawiri; atatuatatu; ndi anayianayi. Amaonjezera mkulenga monga momwe afunira, (palibe chimene chingakanike kwa Iye). Ndithu Allah Ngokhoza chilichonse
❮ Previous Next ❯

Verse in more languages

Transliteration Bangla Bosnian German English Persian French Hindi Indonesian Kazakh Dutch Russian Spanish Turkish Urdu Uzbek