Quran with Chichewa translation - Surah Ya-Sin ayat 43 - يسٓ - Page - Juz 23
﴿وَإِن نَّشَأۡ نُغۡرِقۡهُمۡ فَلَا صَرِيخَ لَهُمۡ وَلَا هُمۡ يُنقَذُونَ ﴾
[يسٓ: 43]
﴿وإن نشأ نغرقهم فلا صريخ لهم ولا هم ينقذون﴾ [يسٓ: 43]
Khaled Ibrahim Betala “Ndipo ngati titafuna tikhoza kuwamiza m’madzi, ndipo sangapezeke wowathandiza, ndiponso sangapulumutsidwe |