Quran with Chichewa translation - Surah Ya-Sin ayat 6 - يسٓ - Page - Juz 22
﴿لِتُنذِرَ قَوۡمٗا مَّآ أُنذِرَ ءَابَآؤُهُمۡ فَهُمۡ غَٰفِلُونَ ﴾
[يسٓ: 6]
﴿لتنذر قوما ما أنذر آباؤهم فهم غافلون﴾ [يسٓ: 6]
Khaled Ibrahim Betala “Kuti uwachenjeze anthu omwe makolo awo sadachenjezedwe; choncho iwo ngoiwala (zomwe zili zofunika kuchitira Allah ndi kudzichitira okha pamodzi ndi anthu ena) |