Quran with Chichewa translation - Surah Ya-Sin ayat 76 - يسٓ - Page - Juz 23
﴿فَلَا يَحۡزُنكَ قَوۡلُهُمۡۘ إِنَّا نَعۡلَمُ مَا يُسِرُّونَ وَمَا يُعۡلِنُونَ ﴾
[يسٓ: 76]
﴿فلا يحزنك قولهم إنا نعلم ما يسرون وما يعلنون﴾ [يسٓ: 76]
Khaled Ibrahim Betala “Mawu awo (onyoza Allah ndi okutsutsa iwe) asakudandaulitse. Ndithu Ife tikudziwa zimene akubisa ndi zimene akuzionetsera poyera |