Quran with Chichewa translation - Surah As-saffat ayat 149 - الصَّافَات - Page - Juz 23
﴿فَٱسۡتَفۡتِهِمۡ أَلِرَبِّكَ ٱلۡبَنَاتُ وَلَهُمُ ٱلۡبَنُونَ ﴾
[الصَّافَات: 149]
﴿فاستفتهم ألربك البنات ولهم البنون﴾ [الصَّافَات: 149]
Khaled Ibrahim Betala “Choncho afunse: “Kodi Mbuye wako ndiye woyenera ana aakazi, ndipo iwo aamuna? (Pomwe iwo akabereka mwana wamkazi amanyansidwa naye)!” |